Salimo 46:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Gonjerani anthu inu, ndipo dziwani kuti ine ndine Mulungu.+Ndidzakwezedwa pakati pa anthu a mitundu ina,+Ndidzakwezedwa padziko lapansi.”+ Ezekieli 36:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 ‘Ndidzayeretsa dzina langa lalikulu+ limene linali kudetsedwa pakati pa mitundu ina ya anthu. Inu munadetsa dzina langalo pakati pa anthu a mitundu ina. Ndikadzayeretsedwa pakati panu, pamaso pa anthu a mitundu inawo, iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.+ Mateyu 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Koma inu muzipemphera motere:+ “‘Atate wathu wakumwamba, dzina+ lanu liyeretsedwe.+
10 “Gonjerani anthu inu, ndipo dziwani kuti ine ndine Mulungu.+Ndidzakwezedwa pakati pa anthu a mitundu ina,+Ndidzakwezedwa padziko lapansi.”+
23 ‘Ndidzayeretsa dzina langa lalikulu+ limene linali kudetsedwa pakati pa mitundu ina ya anthu. Inu munadetsa dzina langalo pakati pa anthu a mitundu ina. Ndikadzayeretsedwa pakati panu, pamaso pa anthu a mitundu inawo, iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.+