Yesaya 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 chotero Yehova adzadula mutu+ ndi mchira+ wa Isiraeli. Adzadulanso mphukira ndi udzu* tsiku limodzi.+ Yesaya 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye wapita kukachisi ndi ku Diboni.+ Wapita kumalo okwezeka kukalira. Mowabu akulira mofuula chifukwa cha Nebo+ ndi Medeba.+ Anthu onse a mmenemo ameta mipala.+ Ndevu za munthu aliyense zametedwa. Yesaya 24:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anthu onse adzachotsedwa ndithu m’dzikolo ndipo katundu yense wa m’dzikolo adzatengedwa,+ pakuti Yehova ndiye wanena mawu amenewa.+
14 chotero Yehova adzadula mutu+ ndi mchira+ wa Isiraeli. Adzadulanso mphukira ndi udzu* tsiku limodzi.+
2 Iye wapita kukachisi ndi ku Diboni.+ Wapita kumalo okwezeka kukalira. Mowabu akulira mofuula chifukwa cha Nebo+ ndi Medeba.+ Anthu onse a mmenemo ameta mipala.+ Ndevu za munthu aliyense zametedwa.
3 Anthu onse adzachotsedwa ndithu m’dzikolo ndipo katundu yense wa m’dzikolo adzatengedwa,+ pakuti Yehova ndiye wanena mawu amenewa.+