-
Yesaya 29:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Anthu inu ndinu opotoka maganizo kwabasi! Kodi woumba zinthu ndi dongo angafanane ndi dongolo?+ Kodi chinthu chochita kupangidwa chingamunene amene anachipanga, kuti: “Iye uja sanandipange”?+ Komanso kodi chinthu chochita kuumbidwa chingamunene amene anachiumba, kuti: “Iye uja sanasonyeze kuti ndi womvetsa zinthu”?+
-