Yobu 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Manja anu omwe ndi amene anandiumba, ndipo anandipanga+Kuzungulira thupi langa lonse, koma tsopano mukufuna kundimeza. Salimo 100:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Dziwani kuti Yehova ndi Mulungu.+Iye ndi amene anatipanga, sitinadzipange tokha.+Ndife anthu ake ndi nkhosa zimene akuweta.+
8 Manja anu omwe ndi amene anandiumba, ndipo anandipanga+Kuzungulira thupi langa lonse, koma tsopano mukufuna kundimeza.
3 Dziwani kuti Yehova ndi Mulungu.+Iye ndi amene anatipanga, sitinadzipange tokha.+Ndife anthu ake ndi nkhosa zimene akuweta.+