Mateyu 5:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 kapena kutchula dziko lapansi chifukwa ndi chopondapo mapazi ake,+ kapena kutchula Yerusalemu chifukwa ndi mzinda+ wa Mfumu yaikulu. Machitidwe 7:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 ‘Kumwamba ndiko mpando wanga wachifumu,+ ndipo dziko lapansi ndilo chopondapo mapazi anga.+ Kodi inu mudzandimangira nyumba yotani? akutero Yehova. Kapena malo oti ine ndipumuliremo ali kuti?+
35 kapena kutchula dziko lapansi chifukwa ndi chopondapo mapazi ake,+ kapena kutchula Yerusalemu chifukwa ndi mzinda+ wa Mfumu yaikulu.
49 ‘Kumwamba ndiko mpando wanga wachifumu,+ ndipo dziko lapansi ndilo chopondapo mapazi anga.+ Kodi inu mudzandimangira nyumba yotani? akutero Yehova. Kapena malo oti ine ndipumuliremo ali kuti?+