-
Levitiko 11:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Pakati pa zamoyo zonse za miyendo inayi, chamoyo chilichonse chokhala ndi mapazi a zikhadabo n’chodetsedwa kwa inu. Aliyense wokhudza chamoyo chimenechi chitafa azikhala wodetsedwa kufikira madzulo.
-