Yohane 16:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Anthu adzakuchotsani m’sunagoge.+ Ndipo nthawi ikubwera pamene aliyense wakupha inu adzaganiza kuti wachita utumiki wopatulika kwa Mulungu.+ Agalatiya 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chifukwa cha abale onyenga+ amene analowa pakati pathu mwakachetechete+ ndiponso mozemba monga akazitape, n’cholinga choti awononge ufulu wathu+ umene tili nawo mogwirizana ndi Khristu Yesu, ndiponso kuti atisandutse akapolo+ . . . 2 Atesalonika 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Wina asakunyengeni pa nkhani imeneyi m’njira iliyonse. Pakuti tsikulo silidzayamba kufika mpatuko+ usanachitike, ndiponso asanaonekere+ munthu wosamvera malamulo,+ amene ndiye mwana wa chiwonongeko.+
2 Anthu adzakuchotsani m’sunagoge.+ Ndipo nthawi ikubwera pamene aliyense wakupha inu adzaganiza kuti wachita utumiki wopatulika kwa Mulungu.+
4 Chifukwa cha abale onyenga+ amene analowa pakati pathu mwakachetechete+ ndiponso mozemba monga akazitape, n’cholinga choti awononge ufulu wathu+ umene tili nawo mogwirizana ndi Khristu Yesu, ndiponso kuti atisandutse akapolo+ . . .
3 Wina asakunyengeni pa nkhani imeneyi m’njira iliyonse. Pakuti tsikulo silidzayamba kufika mpatuko+ usanachitike, ndiponso asanaonekere+ munthu wosamvera malamulo,+ amene ndiye mwana wa chiwonongeko.+