Yohane 17:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Komanso, ine sindikhalanso m’dzikoli pakuti ndikubwera kwa inu, koma iwo adakali m’dzikoli.+ Atate Woyera, ayang’anireni+ chifukwa cha dzina lanu limene mwandipatsa, kuti akhale amodzi mmene ife tilili.+ Yakobo 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kodi si iwo amene amanyoza+ dzina labwino kwambiri limene mukuimira?+
11 “Komanso, ine sindikhalanso m’dzikoli pakuti ndikubwera kwa inu, koma iwo adakali m’dzikoli.+ Atate Woyera, ayang’anireni+ chifukwa cha dzina lanu limene mwandipatsa, kuti akhale amodzi mmene ife tilili.+