Numeri 16:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ndiyeno panabuka moto wochokera kwa Yehova,+ umene unapsereza amuna 250 omwe anali kupereka nsembe zofukiza+ aja. 2 Atesalonika 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pa nthawi imeneyo adzabwezera chilango+ kwa anthu osadziwa Mulungu+ ndi kwa anthu osamvera uthenga wabwino+ wonena za Ambuye wathu Yesu.+
35 Ndiyeno panabuka moto wochokera kwa Yehova,+ umene unapsereza amuna 250 omwe anali kupereka nsembe zofukiza+ aja.
8 Pa nthawi imeneyo adzabwezera chilango+ kwa anthu osadziwa Mulungu+ ndi kwa anthu osamvera uthenga wabwino+ wonena za Ambuye wathu Yesu.+