1 Mafumu 20:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mfumu ya Isiraeli inayankha kuti: “Amuna inu mukamuuze kuti, ‘Musayambe kudzitama nkhondo isanayambe ngati kuti mwapambana kale nkhondoyo.’”+
11 Mfumu ya Isiraeli inayankha kuti: “Amuna inu mukamuuze kuti, ‘Musayambe kudzitama nkhondo isanayambe ngati kuti mwapambana kale nkhondoyo.’”+