Levitiko 16:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Ndiyeno khamu la ana a Isiraeli+ lizim’patsa ana a mbuzi awiri, amphongo, kuti akhale nsembe yamachimo,+ ndi nkhosa yamphongo imodzi kuti ikhale nsembe yopsereza.+
5 “Ndiyeno khamu la ana a Isiraeli+ lizim’patsa ana a mbuzi awiri, amphongo, kuti akhale nsembe yamachimo,+ ndi nkhosa yamphongo imodzi kuti ikhale nsembe yopsereza.+