Amosi 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ine ndimadana ndi zikondwerero zanu ndipo ndikuzikana,+ komanso sindidzasangalala ndi fungo la nsembe zanu zoperekedwa pamisonkhano yanu yapadera.+ Amosi 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inu mukunena kuti: ‘Kodi mwezi watsopano utha liti+ kuti tiyambe kugulitsa chakudya?*+ Komanso sabata+ litha liti kuti tiyambe kuchepetsa muyezo wogulitsira zinthu,+ kukweza mtengo ndi kubera wogula mwa kugwiritsa ntchito masikelo achinyengo?+
21 Ine ndimadana ndi zikondwerero zanu ndipo ndikuzikana,+ komanso sindidzasangalala ndi fungo la nsembe zanu zoperekedwa pamisonkhano yanu yapadera.+
5 Inu mukunena kuti: ‘Kodi mwezi watsopano utha liti+ kuti tiyambe kugulitsa chakudya?*+ Komanso sabata+ litha liti kuti tiyambe kuchepetsa muyezo wogulitsira zinthu,+ kukweza mtengo ndi kubera wogula mwa kugwiritsa ntchito masikelo achinyengo?+