2 Mafumu 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Komanso, inatuma Eliyakimu+ amene anali woyang’anira banja la mfumu, Sebina+ mlembi, ndi akuluakulu a ansembe, onse atavala ziguduli, kuti apite kwa mneneri Yesaya+ mwana wa Amozi.+ 2 Mbiri 29:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Hezekiya+ anakhala mfumu ali ndi zaka 25, ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 29. Mayi ake dzina lawo linali Abiya mwana wa Zekariya.+ 2 Mbiri 32:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma mfumu Hezekiya+ ndi mneneri+ Yesaya+ mwana wa Amozi,+ anali kupempherera nkhani imeneyi+ ndi kufuulira Mulungu kumwamba kuti awapulumutse.+
2 Komanso, inatuma Eliyakimu+ amene anali woyang’anira banja la mfumu, Sebina+ mlembi, ndi akuluakulu a ansembe, onse atavala ziguduli, kuti apite kwa mneneri Yesaya+ mwana wa Amozi.+
29 Hezekiya+ anakhala mfumu ali ndi zaka 25, ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 29. Mayi ake dzina lawo linali Abiya mwana wa Zekariya.+
20 Koma mfumu Hezekiya+ ndi mneneri+ Yesaya+ mwana wa Amozi,+ anali kupempherera nkhani imeneyi+ ndi kufuulira Mulungu kumwamba kuti awapulumutse.+