Yesaya 26:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anthu inu muzidalira Yehova+ nthawi zonse, pakuti Ya* Yehova ndiye Thanthwe+ mpaka kalekale.