Salimo 91:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 91 Aliyense wokhala m’malo otetezeka+ a Wam’mwambamwamba+Adzakhala wosungika mumthunzi wa Wamphamvuyonse.+ Salimo 118:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ya ndiye malo anga obisalapo ndi mphamvu zanga,+Iye amandipulumutsa.+
91 Aliyense wokhala m’malo otetezeka+ a Wam’mwambamwamba+Adzakhala wosungika mumthunzi wa Wamphamvuyonse.+