Salimo 48:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Phiri la Ziyoni limene lili m’dera lakutali la kumpoto,+Ndi lokongola chifukwa lili pamalo okwezeka ndi osangalatsa padziko lonse lapansi,+Mudzi wa Mfumu Yaikulu.+ Zekariya 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Yehova wanena kuti, ‘Ndidzabwerera ku Ziyoni+ ndipo ndidzakhala mu Yerusalemu.+ Yerusalemu adzatchedwadi mzinda wa choonadi+ ndi phiri loyera+ la Yehova+ wa makamu.’”
2 Phiri la Ziyoni limene lili m’dera lakutali la kumpoto,+Ndi lokongola chifukwa lili pamalo okwezeka ndi osangalatsa padziko lonse lapansi,+Mudzi wa Mfumu Yaikulu.+
3 “Yehova wanena kuti, ‘Ndidzabwerera ku Ziyoni+ ndipo ndidzakhala mu Yerusalemu.+ Yerusalemu adzatchedwadi mzinda wa choonadi+ ndi phiri loyera+ la Yehova+ wa makamu.’”