2 Samueli 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Davide anapitiriza kulamulira Isiraeli+ yense ndipo nthawi zonse anali kupereka zigamulo ndi kuchita chilungamo+ kwa anthu ake onse.+ 1 Mafumu 3:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Aisiraeli onse anamva za chigamulo+ chimene mfumu inapereka, ndipo anachita mantha chifukwa cha mfumuyo,+ popeza anaona kuti nzeru+ za Mulungu zinali mwa iye kuti azipereka zigamulo.
15 Davide anapitiriza kulamulira Isiraeli+ yense ndipo nthawi zonse anali kupereka zigamulo ndi kuchita chilungamo+ kwa anthu ake onse.+
28 Aisiraeli onse anamva za chigamulo+ chimene mfumu inapereka, ndipo anachita mantha chifukwa cha mfumuyo,+ popeza anaona kuti nzeru+ za Mulungu zinali mwa iye kuti azipereka zigamulo.