Salimo 33:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Onse okhala padziko lapansi aope Yehova.+Anthu onse okhala panthaka ya dziko lapansi achite naye mantha.+ Salimo 96:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti iye wabwera.+Iye wabwera kudzaweruza dziko lapansi.+Adzaweruza dziko mwachilungamo,+Ndipo adzaweruza mitundu ya anthu mokhulupirika.+ Miyambo 8:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndinali kusangalala ndi nthaka ya dziko lake lapansi,+ ndipo zinthu zimene zinali kundisangalatsa, zinali zokhudzana ndi ana a anthu.+ Yesaya 26:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ife tinali ndi pakati, tinamva zowawa za pobereka,+ koma takhala ngati tabereka mphepo. Palibe chipulumutso chenicheni chimene tapeza m’dzikoli,+ ndipo sitikuberekanso anthu ena oti akhale panthaka ya dziko lapansili.+ Maliro 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mafumu a padziko lapansi ndiponso anthu onse okhala panthaka ya dziko lapansi,+Sanayembekezere kuti mdani angadzalowe pazipata za Yerusalemu.+
8 Onse okhala padziko lapansi aope Yehova.+Anthu onse okhala panthaka ya dziko lapansi achite naye mantha.+
13 Pakuti iye wabwera.+Iye wabwera kudzaweruza dziko lapansi.+Adzaweruza dziko mwachilungamo,+Ndipo adzaweruza mitundu ya anthu mokhulupirika.+
31 Ndinali kusangalala ndi nthaka ya dziko lake lapansi,+ ndipo zinthu zimene zinali kundisangalatsa, zinali zokhudzana ndi ana a anthu.+
18 Ife tinali ndi pakati, tinamva zowawa za pobereka,+ koma takhala ngati tabereka mphepo. Palibe chipulumutso chenicheni chimene tapeza m’dzikoli,+ ndipo sitikuberekanso anthu ena oti akhale panthaka ya dziko lapansili.+
12 Mafumu a padziko lapansi ndiponso anthu onse okhala panthaka ya dziko lapansi,+Sanayembekezere kuti mdani angadzalowe pazipata za Yerusalemu.+