Yesaya 14:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma iweyo watayidwa popanda kuikidwa m’manda,+ ngati mphukira yonyansa imene ili pakati pa anthu akufa ophedwa ndi lupanga, amene akutsikira kumiyala ya m’dzenje.+ Watayidwa ngati mtembo wopondedwapondedwa.+ Ezekieli 29:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwe ndidzakutaya m’chipululu pamodzi ndi nsomba zonse za m’ngalande za Nailo.+ Udzagwera panthaka+ ndipo palibe amene adzakutenge kukakuika m’manda. Ndidzakupereka kwa zilombo zakutchire ndi zolengedwa zouluka kuti ukhale chakudya chawo.+
19 Koma iweyo watayidwa popanda kuikidwa m’manda,+ ngati mphukira yonyansa imene ili pakati pa anthu akufa ophedwa ndi lupanga, amene akutsikira kumiyala ya m’dzenje.+ Watayidwa ngati mtembo wopondedwapondedwa.+
5 Iwe ndidzakutaya m’chipululu pamodzi ndi nsomba zonse za m’ngalande za Nailo.+ Udzagwera panthaka+ ndipo palibe amene adzakutenge kukakuika m’manda. Ndidzakupereka kwa zilombo zakutchire ndi zolengedwa zouluka kuti ukhale chakudya chawo.+