Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 34:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Anthu awo ophedwa adzatayidwa, ndipo fungo loipa la mitembo yawo lidzakwera m’mwamba.+ Mapiri adzasungunuka chifukwa cha magazi awo.+

  • Yeremiya 15:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “‘Ndidzawagwetsera masoka a mitundu inayi,’+ watero Yehova. ‘Ndidzawatumizira lupanga kuti liwaphe, agalu kuti akoke mitembo yawo, zolengedwa zouluka zam’mlengalenga+ ndi zilombo zakutchire kuti ziwadye ndi kuwawononga.

  • Ezekieli 32:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndidzakusiya pamtunda ndiponso ndidzakuponya kuchigwa.+ Ndidzachititsa kuti zolengedwa zonse zouluka m’mlengalenga zitere pa iwe. Ndidzakhutitsa zilombo zakutchire ndi nyama yako.+

  • Chivumbulutso 19:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ndinaonanso mngelo ataimirira padzuwa. Iye anafuula ndi mawu okweza kwa mbalame+ zonse zouluka chapafupi m’mlengalenga, kuti: “Bwerani kuno, dzasonkhaneni ku phwando lalikulu la Mulungu la chakudya chamadzulo,

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena