Yesaya 44:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndimalepheretsa zizindikiro za anthu olankhula zinthu zopanda pake, ndipo ndine amene ndimachititsa olosera kuchita zamisala.+ Ndine amene ndimachititsa anthu anzeru kubwerera kumbuyo, ndiponso amene ndimachititsa nzeru zawo kukhala zopusa.+ 1 Akorinto 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pakuti kwa Mulungu nzeru za m’dzikoli n’zopusa,+ chifukwa Malemba amati: “Iye amakola anzeru m’kuchenjera kwawo.”+
25 Ndimalepheretsa zizindikiro za anthu olankhula zinthu zopanda pake, ndipo ndine amene ndimachititsa olosera kuchita zamisala.+ Ndine amene ndimachititsa anthu anzeru kubwerera kumbuyo, ndiponso amene ndimachititsa nzeru zawo kukhala zopusa.+
19 Pakuti kwa Mulungu nzeru za m’dzikoli n’zopusa,+ chifukwa Malemba amati: “Iye amakola anzeru m’kuchenjera kwawo.”+