Deuteronomo 24:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Uzikumbukira kuti unali kapolo m’dziko la Iguputo, ndipo Yehova Mulungu wako anakuwombola kumeneko.+ N’chifukwa chake ndikukulamula kuti uzichita zimenezi. Yeremiya 31:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti Yehova adzawombola Yakobo,+ ndipo adzamutenganso kumuchotsa m’manja mwa munthu wamphamvu kuposa iyeyo.+
18 Uzikumbukira kuti unali kapolo m’dziko la Iguputo, ndipo Yehova Mulungu wako anakuwombola kumeneko.+ N’chifukwa chake ndikukulamula kuti uzichita zimenezi.
11 Pakuti Yehova adzawombola Yakobo,+ ndipo adzamutenganso kumuchotsa m’manja mwa munthu wamphamvu kuposa iyeyo.+