Yeremiya 13:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ukadzanena mumtima mwako kuti,+ ‘N’chifukwa chiyani zinthu zimenezi zandigwera?’+ pamenepo udzadziwe kuti wavulidwa siketi yako+ ndipo zidendene zako zazunzidwa chifukwa zolakwa zako zachuluka. Mika 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iwe mkazi wokhala ku Safiri tuluka m’dziko lako uli maliseche mochititsa manyazi.+ Mkazi wokhala ku Zaanana sanachoke m’dziko lake. Beti-ezeli anali malo anu othawirako, koma tsopano kuzingomveka kulira kokhakokha.
22 Ukadzanena mumtima mwako kuti,+ ‘N’chifukwa chiyani zinthu zimenezi zandigwera?’+ pamenepo udzadziwe kuti wavulidwa siketi yako+ ndipo zidendene zako zazunzidwa chifukwa zolakwa zako zachuluka.
11 Iwe mkazi wokhala ku Safiri tuluka m’dziko lako uli maliseche mochititsa manyazi.+ Mkazi wokhala ku Zaanana sanachoke m’dziko lake. Beti-ezeli anali malo anu othawirako, koma tsopano kuzingomveka kulira kokhakokha.