Deuteronomo 28:67 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 67 M’mawa udzanena kuti, ‘Zikanakhala bwino akanakhala madzulo!’ ndipo madzulo udzanena kuti, ‘Zikanakhala bwino ukanakhala m’mawa!’ chifukwa cha mantha amene adzagwira mtima wako, ndiponso chifukwa cha zimene maso ako adzaona.+
67 M’mawa udzanena kuti, ‘Zikanakhala bwino akanakhala madzulo!’ ndipo madzulo udzanena kuti, ‘Zikanakhala bwino ukanakhala m’mawa!’ chifukwa cha mantha amene adzagwira mtima wako, ndiponso chifukwa cha zimene maso ako adzaona.+