Yeremiya 30:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova wanena kuti: “Ife tamva phokoso la anthu amene akunjenjemera. Iwo agwidwa ndi mantha+ ndipo palibe mtendere. Amosi 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “‘Tsoka kwa anthu amene akulakalaka tsiku la Yehova!+ Kodi mukuyembekezera chiyani pa tsiku la Yehova anthu inu?+ Limeneli lidzakhala tsiku lamdima osati kuwala,+
5 Yehova wanena kuti: “Ife tamva phokoso la anthu amene akunjenjemera. Iwo agwidwa ndi mantha+ ndipo palibe mtendere.
18 “‘Tsoka kwa anthu amene akulakalaka tsiku la Yehova!+ Kodi mukuyembekezera chiyani pa tsiku la Yehova anthu inu?+ Limeneli lidzakhala tsiku lamdima osati kuwala,+