2 Mafumu 25:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako gulu lonse lankhondo la Akasidi, lomwe linali ndi mkulu wa asilikali olondera mfumu uja, linagwetsa mpanda wonse wa Yerusalemu.+ Nehemiya 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chotero anandiuza kuti: “Anthu otsala amene ali m’chigawo,*+ amene anathawa ku ukapolo, ali pamavuto aakulu+ ndipo akunyozedwa.+ Nawonso mpanda+ wa Yerusalemu unagwa ndipo zipata+ zake zinatenthedwa ndi moto.” Maliro 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova wameza malo okhala a Yakobo. Sanamvere chisoni malo ake alionse.+Mu ukali wake, iye wagwetsa mipanda yolimba kwambiri+ ya mwana wamkazi wa Yuda.Waipitsa ufumu+ ndi akalonga+ ake ndipo wawagwetsera pansi.+
10 Kenako gulu lonse lankhondo la Akasidi, lomwe linali ndi mkulu wa asilikali olondera mfumu uja, linagwetsa mpanda wonse wa Yerusalemu.+
3 Chotero anandiuza kuti: “Anthu otsala amene ali m’chigawo,*+ amene anathawa ku ukapolo, ali pamavuto aakulu+ ndipo akunyozedwa.+ Nawonso mpanda+ wa Yerusalemu unagwa ndipo zipata+ zake zinatenthedwa ndi moto.”
2 Yehova wameza malo okhala a Yakobo. Sanamvere chisoni malo ake alionse.+Mu ukali wake, iye wagwetsa mipanda yolimba kwambiri+ ya mwana wamkazi wa Yuda.Waipitsa ufumu+ ndi akalonga+ ake ndipo wawagwetsera pansi.+