-
Ezekieli 17:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 “Ndiyeno unene kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Kodi mtengo umenewu zinthu zidzauyendera bwino?+ Kodi munthu wina sadzadula mizu yake+ ndi kuwononga zipatso zake? Kodi mphukira zake zimene zangothyoledwa kumene sizidzauma?+ Mtengowo udzauma ndithu. Sudzachita kufuna dzanja lamphamvu kapena anthu ambiri kuti uzulidwe ndi mizu yomwe.
-