Yesaya 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndamva Yehova wa makamu akulumbira kuti nyumba zambiri, ngakhale zitakhala zikuluzikulu ndiponso zabwino, zidzakhala chinthu chodabwitsa kwambiri ndipo zidzakhala zopanda wokhalamo.+ Amosi 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, sangachite kalikonse asanaulule chinsinsi chake kwa atumiki ake, aneneri.+
9 Ndamva Yehova wa makamu akulumbira kuti nyumba zambiri, ngakhale zitakhala zikuluzikulu ndiponso zabwino, zidzakhala chinthu chodabwitsa kwambiri ndipo zidzakhala zopanda wokhalamo.+
7 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, sangachite kalikonse asanaulule chinsinsi chake kwa atumiki ake, aneneri.+