Yobu 40:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mkwiyo wako wosefukira utuluke,+Ndipo uone aliyense wodzikweza n’kumutsitsa. Salimo 75:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mulungu ndiye woweruza.+Amatsitsa wina ndi kukweza wina.+ Luka 1:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Watsitsa anthu amphamvu+ zawo pamipando yachifumu, ndipo wakweza anthu wamba.+