Miyambo 29:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Munthu wodzudzulidwa kawirikawiri+ koma amene amaumitsa khosi lake,+ adzathyoledwa mwadzidzidzi ndipo akadzatero sadzachira.+ Yesaya 48:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Podziwa kuti ndinu olimba,+ ndi kuti mtsempha wa khosi lanu uli ngati chitsulo,+ ndiponso kuti mphumi yanu ili ngati mkuwa,+
29 Munthu wodzudzulidwa kawirikawiri+ koma amene amaumitsa khosi lake,+ adzathyoledwa mwadzidzidzi ndipo akadzatero sadzachira.+
4 Podziwa kuti ndinu olimba,+ ndi kuti mtsempha wa khosi lanu uli ngati chitsulo,+ ndiponso kuti mphumi yanu ili ngati mkuwa,+