Yeremiya 26:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mwina adzamvera ndipo aliyense wa iwo adzabwerera kuchoka panjira yake yoipa.+ Pamenepo ndidzasintha maganizo anga pa tsoka limene ndikufuna kuwagwetsera chifukwa cha zochita zawo zoipa.+ Mika 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Choncho Yehova wanena kuti, ‘Ndikuganiza zobweretsa tsoka pa banja ili.+ Tsoka+ limenelo simudzatha kulipewa,+ moti anthu inu simudzayendanso modzikuza+ chifukwa idzakhala nthawi ya tsoka.+
3 Mwina adzamvera ndipo aliyense wa iwo adzabwerera kuchoka panjira yake yoipa.+ Pamenepo ndidzasintha maganizo anga pa tsoka limene ndikufuna kuwagwetsera chifukwa cha zochita zawo zoipa.+
3 “Choncho Yehova wanena kuti, ‘Ndikuganiza zobweretsa tsoka pa banja ili.+ Tsoka+ limenelo simudzatha kulipewa,+ moti anthu inu simudzayendanso modzikuza+ chifukwa idzakhala nthawi ya tsoka.+