Salimo 35:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma moyo wanga ukondwere mwa Yehova.+Usangalale chifukwa cha chipulumutso chake.+ Salimo 109:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Pakuti adzaima kudzanja lamanja la munthu wosauka,+Kuti am’pulumutse kwa omuweruza mopanda chilungamo.
31 Pakuti adzaima kudzanja lamanja la munthu wosauka,+Kuti am’pulumutse kwa omuweruza mopanda chilungamo.