25 ‘Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti: “Iwe watumiza makalata m’dzina lako+ kwa anthu onse amene ali ku Yerusalemu, kwa Zefaniya+ mwana wa Maaseya, wansembe, ndi kwa ansembe onse. Makalatawo ndi onena kuti,
3 Mfumu Zedekiya inatumiza Yehukali+ mwana wa Selemiya ndi Zefaniya+ mwana wa Maaseya+ wansembe kwa mneneri Yeremiya ndi uthenga wakuti: “Chonde, tipempherere kwa Yehova Mulungu wathu.”+