2 Mbiri 28:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pa nthawi imene Mfumu Ahazi inali kusautsidwa, inawonjezera kuchita zosakhulupirika kwa Yehova.+ Yesaya 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anthuwo sanabwerere kwa amene akuwamenya+ ndipo sanafunefune Yehova wa makamu,+