Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 33:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Isiraeli adzakhala motetezeka,+

      Kasupe wa Yakobo adzakhala mosatekeseka,+

      M’dziko lokhala ndi chakudya ndi vinyo watsopano.+

      Ndipo kumwamba kwake kudzagwetsa mame.+

  • Salimo 130:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Isiraeli ayembekezere Yehova,+

      Pakuti Yehova amasonyeza kukoma mtima kosatha.+

      Iye ali ndi mphamvu zochuluka zowombolera anthu ake.+

  • Yesaya 62:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Sudzatchedwanso mkazi wosiyidwa mpaka kalekale+ ndipo dziko lako silidzatchedwanso labwinja.+ Koma iweyo dzina lako lidzakhala “Ndimakondwera Naye,”+ ndipo dziko lako lidzatchedwa “Mkazi Wokwatiwa.” Pakuti Yehova adzakondwera nawe ndipo dziko lako lidzakhala ngati mkazi wokwatiwa.+

  • Yeremiya 32:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 ‘Inetu ndikuwasonkhanitsa pamodzi kuchokera kumayiko onse kumene ndinawabalalitsira nditakwiya, kupsa mtima ndiponso ndili ndi ukali waukulu.+ Ndidzawabwezeretsa m’dziko lino ndi kuwachititsa kukhala mwamtendere.+

  • Zekariya 14:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Anthu adzakhala mumzindawo ndipo simudzakhalanso zinthu zoyenera kuwonongedwa.+ Anthu okhala mu Yerusalemu, adzakhala mmenemo ali otetezeka.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena