Salimo 35:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Njira yawo ikhale ya mdima ndi yoterera,+Ndipo mngelo wa Yehova aziwathamangitsa. Salimo 73:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndithudi, mwawaimika pamalo oterera.+Mwawagwetsa kuti awonongeke.+ Miyambo 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Njira ya oipa ili ngati mdima.+ Iwo sadziwa chimene chimawapunthwitsa.+ Yeremiya 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Patsani Yehova Mulungu wanu ulemerero+ asanachititse mdima,+ komanso mapazi anu asanapunthwe pamapiri madzulo dzuwa litalowa.+ Mudzayembekeza kuwala+ koma iye adzabweretsa mdima,+ ndipo adzachititsa mdima wandiweyani.+
16 Patsani Yehova Mulungu wanu ulemerero+ asanachititse mdima,+ komanso mapazi anu asanapunthwe pamapiri madzulo dzuwa litalowa.+ Mudzayembekeza kuwala+ koma iye adzabweretsa mdima,+ ndipo adzachititsa mdima wandiweyani.+