Deuteronomo 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 ndipo chizindikiro kapena chodabwitsa chimenecho chachitikadi,+ chimene anachita ponena kuti, ‘Tiyeni titsatire milungu ina imene simunaidziwe, ndipo tiitumikire,’ Machitidwe 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma Elima, wamatsenga, (uku ndiye kumasulira kwa dzina lakeli) anayamba kutsutsana nawo.+ Iye anali kuyesetsa kuti bwanamkubwayo asakhulupirire Ambuye.
2 ndipo chizindikiro kapena chodabwitsa chimenecho chachitikadi,+ chimene anachita ponena kuti, ‘Tiyeni titsatire milungu ina imene simunaidziwe, ndipo tiitumikire,’
8 Koma Elima, wamatsenga, (uku ndiye kumasulira kwa dzina lakeli) anayamba kutsutsana nawo.+ Iye anali kuyesetsa kuti bwanamkubwayo asakhulupirire Ambuye.