2 Samueli 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Abisalomu anapitiriza kuchita zinthu zoterezi kwa Aisiraeli onse amene anali kubwera kwa mfumu kuti iwaweruzire milandu yawo, moti Abisalomu anapitiriza kukopa mitima ya anthu a mu Isiraeli.+ Salimo 50:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iwe umadana ndi malangizo,*+Ndipo umaponya mawu anga kunkhongo.+
6 Abisalomu anapitiriza kuchita zinthu zoterezi kwa Aisiraeli onse amene anali kubwera kwa mfumu kuti iwaweruzire milandu yawo, moti Abisalomu anapitiriza kukopa mitima ya anthu a mu Isiraeli.+