Ezekieli 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Amuna inu, kodi masomphenya mwaonawa si abodza? Kodi zimene mwaloserazi si zonama? Inu mwati, ‘Yehova wanena kuti,’ pamene ine sindinalankhule kalikonse.”’+
7 Amuna inu, kodi masomphenya mwaonawa si abodza? Kodi zimene mwaloserazi si zonama? Inu mwati, ‘Yehova wanena kuti,’ pamene ine sindinalankhule kalikonse.”’+