Yeremiya 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma ine ndinakubzala ngati mtengo wa mpesa wofiira, wabwino kwambiri.+ Mtengo wonsewo unali mbewu yeniyeni yabwino. Ndiye wandisinthira bwanji kukhala mphukira yachabechabe ya mtengo wa mpesa wachilendo?’+ Yeremiya 2:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 N’chifukwa chiyani kusintha njira kwako ukukuona mopepuka?+ Udzachitanso manyazi ndi Iguputo+ monga mmene unachitira manyazi ndi Asuri.+
21 Koma ine ndinakubzala ngati mtengo wa mpesa wofiira, wabwino kwambiri.+ Mtengo wonsewo unali mbewu yeniyeni yabwino. Ndiye wandisinthira bwanji kukhala mphukira yachabechabe ya mtengo wa mpesa wachilendo?’+
36 N’chifukwa chiyani kusintha njira kwako ukukuona mopepuka?+ Udzachitanso manyazi ndi Iguputo+ monga mmene unachitira manyazi ndi Asuri.+