Ezekieli 18:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “‘Anthu inu mudzanena kuti: “Njira za Yehova n’zopanda chilungamo.”+ Tamverani inu a nyumba ya Isiraeli. Kodi njira zanga ndiye zopanda chilungamo?+ Kodi njira za anthu inu sindizo zopanda chilungamo?+
25 “‘Anthu inu mudzanena kuti: “Njira za Yehova n’zopanda chilungamo.”+ Tamverani inu a nyumba ya Isiraeli. Kodi njira zanga ndiye zopanda chilungamo?+ Kodi njira za anthu inu sindizo zopanda chilungamo?+