2 Samueli 13:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako Tamara anadzithira phulusa+ kumutu ndi kung’amba malaya ake amizeremizere aja. Ndiyeno anaika manja ake pamutu+ n’kunyamuka kumapita, akulira.
19 Kenako Tamara anadzithira phulusa+ kumutu ndi kung’amba malaya ake amizeremizere aja. Ndiyeno anaika manja ake pamutu+ n’kunyamuka kumapita, akulira.