Yeremiya 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yeremiya analandira mawu ochokera kwa Yehova m’masiku a Yosiya+ mwana wa Amoni.+ Yosiya anali mfumu ya Yuda, ndipo Yeremiya analandira mawuwo m’chaka cha 13 cha ulamuliro wa Yosiyayo.+
2 Yeremiya analandira mawu ochokera kwa Yehova m’masiku a Yosiya+ mwana wa Amoni.+ Yosiya anali mfumu ya Yuda, ndipo Yeremiya analandira mawuwo m’chaka cha 13 cha ulamuliro wa Yosiyayo.+