Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 23:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Kuwonjezera apo, Farao Neko anaika Eliyakimu+ mwana wa Yosiya kukhala mfumu m’malo mwa Yosiya bambo ake, n’kumusintha dzina kuti akhale Yehoyakimu. Atatero anatenga Yehoahazi n’kupita naye ku Iguputo, kumene anakafa pamapeto pake.+

  • 2 Mbiri 36:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Kuwonjezera apo, mfumu+ ya Iguputo inaika Eliyakimu+ m’bale wa Yehoahazi kukhala mfumu ya Yuda ndi Yerusalemu n’kumusintha dzina kuti akhale Yehoyakimu. Koma Yehoahazi m’bale wakeyo, Neko+ anam’tenga n’kupita naye ku Iguputo.+

  • Yeremiya 1:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Mawuwo anapitiriza kufika kwa Yeremiya m’masiku a Yehoyakimu+ mfumu ya Yuda, mwana wa Yosiya, mpaka m’chaka cha 11, kumapeto kwa ulamuliro wa Zedekiya+ mfumu ya Yuda, mwana wa Yosiya, pamene anthu a mu Yerusalemu anatengedwa kupita ku ukapolo m’mwezi wachisanu.*+

  • Yeremiya 25:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Awa ndi mawu amene Yeremiya anauzidwa onena za anthu onse a mu Yuda m’chaka chachinayi cha ulamuliro wa Yehoyakimu+ mwana wa Yosiya, mfumu ya Yuda, chimenenso chinali chaka choyamba cha ulamuliro wa Nebukadirezara mfumu ya Babulo.

  • Yeremiya 35:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 M’masiku a Yehoyakimu+ mwana wa Yosiya, mfumu ya Yuda, Yehova anauza Yeremiya kuti:

  • Yeremiya 36:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Ndiyeno m’chaka chachinayi cha ulamuliro wa Yehoyakimu+ mwana wa Yosiya, mfumu ya Yuda, Yehova anauza Yeremiya kuti:

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena