Yoswa 9:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Tsopano tadzipereka m’manja mwanu. Muchite nafe chilichonse chimene mukuona kuti n’chabwino ndi choyenera kwa inu.”+ Yeremiya 38:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno Mfumu Zedekiya inawayankha kuti: “Taonani! Iye ali m’manja mwanu. Palibe chimene ine mfumu ndingachite motsutsana nanu.”+
25 Tsopano tadzipereka m’manja mwanu. Muchite nafe chilichonse chimene mukuona kuti n’chabwino ndi choyenera kwa inu.”+
5 Ndiyeno Mfumu Zedekiya inawayankha kuti: “Taonani! Iye ali m’manja mwanu. Palibe chimene ine mfumu ndingachite motsutsana nanu.”+