1 Mafumu 19:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho Eliya anachita mantha moti ananyamuka n’kuyamba kuthawa kuti apulumutse moyo wake,+ mpaka anakafika ku Beere-seba+ wa ku Yuda.+ Mtumiki wake anamusiya kumeneko, Miyambo 29:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kuopa anthu n’kumene kumatchera msampha,+ koma wokhulupirira Yehova adzatetezedwa.+ Mateyu 10:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Musachite mantha+ ndi amene amapha thupi koma sangaphe moyo, m’malomwake, muziopa iye+ amene angathe kuwononga zonse ziwiri, moyo ndi thupi lomwe m’Gehena.*+
3 Choncho Eliya anachita mantha moti ananyamuka n’kuyamba kuthawa kuti apulumutse moyo wake,+ mpaka anakafika ku Beere-seba+ wa ku Yuda.+ Mtumiki wake anamusiya kumeneko,
28 Musachite mantha+ ndi amene amapha thupi koma sangaphe moyo, m’malomwake, muziopa iye+ amene angathe kuwononga zonse ziwiri, moyo ndi thupi lomwe m’Gehena.*+