Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 23:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Uthenga wokhudza Turo:+ Lirani mofuula inu zombo za ku Tarisi,+ chifukwa chakuti mzindawo wasakazidwa ndipo sulinso doko. Sulinso malo oti mungafikepo.+ Anthu amva zimenezi ali kudziko la Kitimu.+

  • Yeremiya 47:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Iwo adzachita mantha chifukwa cha tsiku limene likubwera. Tsikuli ndi lofunkha zinthu za Afilisiti+ onse ndi kupha wopulumuka aliyense wothandiza+ Turo+ ndi Sidoni.+ Pakuti Yehova adzafunkha zinthu za Afilisiti+ amene atsala ochokera pachilumba cha Kafitori.+

  • Ezekieli 26:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pa chifukwa chimenechi, Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Ine ndikuukira iwe Turo ndipo ndikutumizira mitundu yambiri ya anthu+ kuti idzamenyane nawe. Anthuwo adzabwera ngati mafunde a m’nyanja.+

  • Amosi 1:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndidzatumiza moto pakhoma la Turo ndipo udzanyeketsa nsanja zake zokhalamo.’+

  • Zekariya 9:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Turo anamanga chiunda chomenyerapo nkhondo.* Anadziunjikira siliva wochuluka ngati dothi ndiponso golide wochuluka ngati matope a m’misewu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena