Salimo 136:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anawatulutsa ndi dzanja lamphamvu ndi mkono wotambasula:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale. Yeremiya 32:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Kalanga ine! Inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa.+ Inuyo ndi amene munapanga kumwamba ndi dziko lapansi pogwiritsa ntchito mphamvu yanu+ ndi dzanja lanu lotambasula.+ Nkhaniyi si yovuta kwa inu.+
12 Anawatulutsa ndi dzanja lamphamvu ndi mkono wotambasula:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale. Yeremiya 32:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Kalanga ine! Inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa.+ Inuyo ndi amene munapanga kumwamba ndi dziko lapansi pogwiritsa ntchito mphamvu yanu+ ndi dzanja lanu lotambasula.+ Nkhaniyi si yovuta kwa inu.+
17 “Kalanga ine! Inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa.+ Inuyo ndi amene munapanga kumwamba ndi dziko lapansi pogwiritsa ntchito mphamvu yanu+ ndi dzanja lanu lotambasula.+ Nkhaniyi si yovuta kwa inu.+