Miyambo 1:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Koma munthu wondimvera adzakhala mwabata+ ndipo sadzasokonezeka chifukwa choopa tsoka.”+ Yeremiya 38:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma Yeremiya anati: “Sadzakuperekani m’manja mwawo mwa njira imeneyo. Chonde, mverani mawu a Yehova amene ndikukuuzani. Mukatero, zinthu zidzakuyenderani bwino+ ndipo mudzakhalabe ndi moyo.
20 Koma Yeremiya anati: “Sadzakuperekani m’manja mwawo mwa njira imeneyo. Chonde, mverani mawu a Yehova amene ndikukuuzani. Mukatero, zinthu zidzakuyenderani bwino+ ndipo mudzakhalabe ndi moyo.