Yeremiya 28:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pa zaka ziwiri zokha ndibwezeretsa pamalo ano ziwiya zonse za m’nyumba ya Yehova zimene Nebukadinezara mfumu ya Babulo+ anatenga pamalo ano ndi kupita nazo ku Babulo.’”
3 Pa zaka ziwiri zokha ndibwezeretsa pamalo ano ziwiya zonse za m’nyumba ya Yehova zimene Nebukadinezara mfumu ya Babulo+ anatenga pamalo ano ndi kupita nazo ku Babulo.’”